Timu ya Karonga United yamenya ndi kutulutsa timu ya Mighty Wanderers mu masewelo a quarter final yachiwiri ya chikho cha Airtel Top 8 omwe anachitikira pa bwalo la Karonga. Wanderers inayamba masewelowa ili ndi chigoli chimodzi mthumba koma chigawo choyamba chinatha osabala kanthu ngakhale ma timu awiriwa anayesetsa kupeza mipata ingapo yomwe sinaphule chigoli. Pa […]
The post Karonga United yakaniza Wanderers ndalama za Airtel Top 8 appeared first on Malawi 24.