Ngati njira imodzi yokopera alimi kuti akagulitse chimanga chawo ku bungwe logula ndikugulitsa mbewu la ADMARC, bungweli lakweza mtengo omwe likugulira chimanga. Malingana ndi chi kalata chomwe tawona, bungweli lidzigula chimanga pa mtengo wa K700 pa kilogalamu imodzi, kuchoka pa K650 pa kilogalamu imodzi. Izi zikutanthauza kuti bungweli pano lidziwagula alimi thumba lolemera ma kilogalamu […]
The post ADMARC yakweza mtengo ogulira chimanga appeared first on Malawi 24.