Zina ukamva kukamwa yasa, anthu okhala m'mudzi mwa Phanisa m'boma la Mulanje usiku wathawu agenda ndi kuvulaza alendo okawona phiri powaganizira kuti amakayika zipangizo zomwe zibweretse namondwe wa Chido m'phiri la Mulanje. M'neneli wa apolisi Ku Mulanje watsimikizira wailesi ina m'dziko muno ponena kuti anthu okwiyawa aphwanya Ambulance ya pa chipatala cha Mulanje mission pamene […]
The post Agendedwa ku Mulanje powaganizira kuti afuna kubweretsa namondwe wa Chido appeared first on Malawi 24.