Mkulu wa bungwe lomenyera ufulu anthu mdziko muno la Centre for Democracy and Economic Development Initiatives (CDEDI), Sylvester Namiwa wati aMalawi akumanidwa Vitamin A ndi michere ina yomwe imapezeka mu Suga ndipo ndi yofunika kwambiri chifukwa cha ukambelembele omwe wazungulira malonda a Suga mdziko muno. A Namiwa awuza nduna yowona za malonda a Vitumbiko Mumba […]
The post AMalawi mukuwamana Vitamin A - Namiwa appeared first on Malawi 24.