Namwino wapachipatala cha Mchinji, Bertha Kanyinji walimbikitsa a namwino amzake mdziko muno kugwira ntchito modzipeleka komaso kutsatila malamulo a ntchito nthawi zonse panthawi ya ntchito. Kanyinji wayankhula izi atasankhidwa komaso kukwezedwa udindo ndimtsogoleri wadziko lino, Lazarus Chakwera ngati Namwino yemwe wagwira ntchito mwapamwamba m'boma la Mchinji. Pa mwambo okumbukira a namwino pa dziko lonse lapansi […]
The post Anamwino tidzilemekeza ntchito yathu - Bertha Kanyinji appeared first on Malawi 24.