Apolisi m'boma la Chiradzulu amanga anthu okwana 15 ochokela m'mudzi wa Chitera powaganizila kuti aphwanya ndi kuba katundu wa ndalama zopitilira 23 miliyoni kwacha pa Chikale esiteti yomwe ndi ya Mulli Brothers. Malinga ndi mneneri wa a polisi ku Chiradzulu a Cosmas Kagulo, anthuwa anachita izi pokwiya ndi poganiza kuti mzawo wina anamangidwa chifukwa cha […]
The post Anthu 15 amangidwa chifukwa chowononga katundu wa ndalama zokwana K23 miliyoni appeared first on Malawi 24.