Apolisi m'boma la Mulanje akhazikitsa ntchito yosakasaka munthu yemwe akumuganizira kuti wapha mzake atamugwira akuba therere m'munda mwake. Mneneri wa apolisi m'bomali, Innocent Moses, wati izi zachitika usiku wa Lamulungu m'mudzi mwa Gojo kwa mfumu Mthiramanja. 'Thupi la Piyasi Ligomeka linapezeka m'munda lili ndi mabala aakulu. Woganiziradwayu anabwereka munda wa wophedwayu ndikubzalamo therere logulitsa. Ndipo […]
The post Apha munthu chifukwa cha thelere appeared first on Malawi 24.