Apolisi ku Ntcheu amanga a Joseph Gamaliyele a zaka makumi awiri ndi mphambu zisanu, 29, powaganizira kuti agwililira mtsikana wazaka makumi awiri ndi mphambu zitatu. Malingana ndi m'neneri wa a Polisi ku Ntcheu a Rabbeca Kwisongole ati mzimayiyu ndi nkhosa ya mu utumiki wa Ebenezer Niss . 'Lolemba pa December 20, 2021 mayiyu anapita ku […]
The post Apolisi amanga m’neneri kamba komuganizira kuti anagwililira appeared first on Malawi 24.