Wachiwiri kwa mtsogoleri was dziko lino a Micheal Usi ati mipingo ikuyenelera osalema kupemphelera atsogoleri komanso ndi adindo onse kuti asamatengeke ndi zinthu kuyiwala chomwe analumbira kuti adzachitira anthu uku atagwira baibulo kapena Quran. A Usi amayankhula izi ku Malamulo m'boma la Thyolo lero pamene anakakhala nawo pa mapemphero a tsiku lasabata. M'mau ake wachiwiri […]
The post Atsogoleri tiwaikize m'mapephero pa tchimo la dyera - Usi appeared first on Malawi 24.