M'modzi mwa omenyera ufulu wa anthu mdziko muno a Bon Kalindo ati zomwe anayankhula akuluakulu ena a chipani cha Democratic Progressive (DPP) ku msonkhano wa ndale ku Ndirande mu mzinda wa Blantyre ndi zokolezera udani komanso ndi khalidwe lonunkha pamene nkhondo yolimbana ndi udani ndi nkhanza pa ndale ili mkati. Poyankhula mu uthenga wawo omwe […]
The post Bon kalindo wati DPP yapanga khalidwe lonunkha ku Ndirande appeared first on Malawi 24.