Bungwe la Malawi Bureau of Standards (MBS) lati likhala likupanga chipikisheni mu misika komanso mawokala wonse m’dziko muno pofuna kuchotsa pa msika mitundu ya machesi omwe sanavomelezedwe ndi bungweli. M’chikatala chomwe bungweli latulutsa chati mitundu yina ya machesi monga Paka, Tinga, Kasuku , Mo komanso Soccer yomwe ikupezeka pa misika ya m’dziko muno siyili mukawundula […]
The post Bungwe la MBS lati lipanga chipikisheni cha machesi osavomerezeka pa msika appeared first on Malawi 24.