Bwalo la milandu munzinda wa Lilongwe lalamura kuti Prophet Shepherd Bushiri komanso mkazi wake Mary, atumizidwe mdziko la South Africa kuti akayankhe milandu yokhudza ndalama komanso yogwililira yomwe akuganizilidwa. Koma awiri ati akachita apilo chigamulochi. Popeleka chigamulochi, Senior Resident Magistrate Madalitso Chimwaza adalamula kuti awiriwa akasungidwe kaye kundende podikira kuwatumiza ku South Africa kukayankha milandu […]
The post Bushiri atumizidwe ku South Africa - Khothi lagamula appeared first on Malawi 24.