…wayitanitsa zionetsero ku Mulanje A Bon Kalindo ati zomwe zikuchitika pankhani yakumangidwa kwa mkulu wa ACB a Martha Chizuma, ndi chinyenga aphunzitsi ndipo ati zili ngati mfiti yomwe imamupha munthu ndipo yomweyo imakaliraso kwambiri pa maliro a munthu yamuphayo kuti isadziwike kuti yapha ndiiyo. A Kalindo amayankhula izi potsatira zomwe anayankhula mtsogoleri wa dziko lino […]
The post Chakwera akufuna kuchotsa Chizuma kudzera mwa anthu ena – Kalindo appeared first on Malawi24.