A Kondwani Nankhumwa omwe ndi mtsogoleri wachipani cha People's Development Party (PDP) ati ankapingidwapingidwa m’mene iwo anali membala wa chipani cha Democratic Progressive Party (DPP) kamba koti mamembala ena mchipanichi amazindikila kuti iwo akagonjetsa a Peter Mutharika mwayi opita ku msonkhano waukulu okasankha atsogoleri m'ma udindo ukapezeka. Iwo adayankhula izi pa bwalo la Masintha mu […]
The post Ine ndinakagonjetsa a Mutharika ku convention – Nankhumwa appeared first on Malawi 24.