Okonda masewero a mpira wa miyendo anangoti kukamwa yasa Lamulungu pa bwalo la Mulanje Park pomwe wosewera wa FOMO FC ndi wina wa Premier Bet Dedza Dynamos anakana kutuluka m'bwalo la za masewero kupita kokapumulira mpaka onse kuonetsedwa makhadi ofiyira. Lamulungu pa 23 June 2024, timu ya FOMO FC inalandira pa bwalo la Mulanje Park […]
The post Juju! Wosewera wa FOMO, Dedza Dynamos akana kutuluka m'bwalo appeared first on Malawi 24.