Pomwe pali kusamvana pa nkhani yamalipiro pakati pa achinyamata omwe akugwira ntchito mdziko la Israel ndi ma agent omwe adawatumiza mdzikolo, boma kudzera mwa Kazembe woimila Malawi ku Israel lati achinyamata omwe sakufuna kuti ndalama zawo zidzilowa ku banki, anene ndipo ndege yowabweletsa kuno kumpanje ilipo kale. Nkhaniyi yayamba pomwe achinyamata ena omwe ali mdziko […]
The post Malipilo ku Israel: boma lati amene sakufuna asiye, apeleke mwayi kwa ena appeared first on Malawi 24.