Mphungu wakumadzulo kwa mzinda wa Lilongwe, George Zulu wati alibe mantha ndi aliyense patsogolo pazisankho zachipulura za chipani cha Kongeresi. Zulu amayankhula izi kutsatila zipolowe zomwe zinachitika pakati paotsatila Kongeresi, omwe akuganiziridwa kuti ndi otsatila ake komanso yemwe akufuna kupikisana naye dela la Mtandire Mtsiriza, Ruth Chingwalu. Koma poyankhapo pa nkhaniyi, Zulu watsutsa kuti zipolowezi […]
The post Ndilibe mantha ndi aliyense - Zulu appeared first on Malawi 24.