Apolisi munzinda wa Lilongwe atsimikiza kuti nzika ya m’dziko la Britain ya zaka 26 yabedwa ndi anthu osadziwika pomwe imachokera ku mapemphero Lolemba masana. Malingana ndi ofalitsa nkhani za polisi ya Lilongwe a Hastings Chigalu, nzika ya ku Britain-yi yazindikilidwa ngati a Muhammad Kasman, omwe ndi m'modzi mwa akuluakulu ogwira ntchito ku Universal Industries. Chigalu […]
The post Nzika ya ku Britain yabedwa ku Lilongwe appeared first on Malawi 24.