Pomwe anthu omwe anaononga katundu wa chipani cha DPP ndikuvulaza mamembala ena a chipanichi ku Lilongwe sanamangidwebe mpaka pano, apolisi ku Phalombe dzulo anathila unyolo membala wa chipani cha DPP yemwe akufuna kudzapikisana nawo pa mpando wa phungu kum’mwera kwa bomalo, kamba kouza otsatira chipanichi kuti ku Phalombe ndi kwa DPP ndipo asalore chipani cha […]
The post Shado wa DPP wapatsidwa belo kutsatila kumangidwa kwake atauza anthu kuti asalole MCP kufika ku Phalombe appeared first on Malawi 24.