Phungu wa nyumba ya malamulo wa dela la Lilongwe Mapuyu South Esther Cecilia Kathumba ati akapita kunyumba ya malamulo akawupanga mpando wa mtsogoleri wa dziko kuti ukakhale wa muyaya ndipo kuti a Lazarus Chakwera adzapitilize kutsogolera dziko la Malawi kupitilira 2030 komanso kuti a Chakwera adzausiye mpandowu mwa kufuna kwawo chifukwa cha ukalamba. Phunguyu wayankhula […]
The post Tikakonze malamulo Chakwera apitilize kuposela 2030 - Kathumba appeared first on Malawi 24.