Khamu la anthu ochokera m'mudzi wa Mujinge mfumu yayikulu M'mbelwa m'boma la Mzimba lakhamukira ku polisi ya Mzimba komwe akufuna kuti a polisi atulutse sing'anga wawo yemwe akuti amachotsa ufuti mwa anthu m'mudzimo. Sing'angayo yemwe akudziwika kuti Nyauzimu Gondwe akuti anachokera m'boma la Rumphi kubwera m'mudzi wa Mujinge atayitanidwa ndi anthu limodzi ndi mafumu a […]
The post Titulitsireni ng'anga yathu, amang'ara anthu ku Mzimba appeared first on Malawi 24.