Pomwe anthu anali ndichiyembekezo kuti zinthu zambiri zitha kuyamba kuyenda bwino kaamba ka ndalama yokwana K7 thililiyoni yomwe bungwe lakunja la Bridgin Foundation limayenera kupeleka ku dziko lino, nduna ya zachuma a Sosten Gwengwe athira mchenga mu mmemo wagulo ponena kuti mgwirizanowu unali zamkutu zenizeni. Pa 28 November chaka chatha a Gwengwe anasainira mgwirizano ndi […]
The post Zamkutu! Gwengwe wati a Malawi ayiwale za K7 thililiyoni ya Bridgin appeared first on Malawi24.