Bwalo la Bingu mu mzinda wa Lilongwe lero lakwanitsa kutulutsa ndalama za nkhani-nkhani zokwana 113 million Kwacha kuchokera mu masewelo amodzi a Silver Strikers ndi FCB Nyasa Big Bullets. Masewelowa omwe anali otsekulira season ya 2025 ya mpikisano wa TNM Super League, apanga mbiri pomwe chitsekulireni bwaloli m'chaka cha 2017 izi sizidachitikepo. Wachiwiri kwa mtsogoleri […]
The post 113 million Kwacha pa masewelo a Silver ndi Bullets appeared first on Malawi 24.