Apolisi ku Lilongwe amanga abambo atatu omwe akuwaganizira kuti akhala akuba m'mashopu ndi m’manyumba osatha kumanga ku dera la Chitipi. Malingana ndi wachiwiri kwa m'neneri wa polisi ya Lilongwe, a Khumbo Sanyiwa, anthuwa anaba ma belo a sugar, zitseko, mafosholo, ma felemu azitseko, ndi matumba achimanga mwazina, zokwana K3.4 million. Zadziwika kuti anthuwa ndi a […]
The post Abambo atatu anjatidwa powaganizira kuti ndiakuba ku Lilongwe appeared first on Malawi 24.