Njonda ziwiri ku Manja munzinda wa Blantyre, zabzala chinangwa kamba kochita chibwana cha mchombo lende kukonkha chakumwa choyankhulitsa chizungu ku mimba kukulira malikhwelu. Malingana ndi wofalitsa nkhani ku polisi ya Soche, Aaron Chilala, Vincent Chotokoma wazaka 21, yemwe ankagulitsa nsapato ku Limbe, kumathero a sabata yatha adawonedwa akukonkha bibida ngati kulibe mawa chosecho akuti adali […]
The post Afa atamwa osadyera appeared first on Malawi 24.