Bungwe la National Economic Empowerment Fund (NEEF) ladandaula ndikuchepa kwa anthu omwe akufuna thandizo la ngongole. Mkulu wa bungweli ku Mponela, Lloyd Nyakamela ndiye wanena izi Lachitatu pamwambo opeleka ngongole ya zipangizo za ulimi ku gulu la Mtanga, Mfumu yaikulu Njombwa ku Kasungu. Bungwe la NEEF, lapeleka matumba 100 a feteleza, mbewu makilogalamu 500, ndizipangizo […]
The post Anthu ofuna thandizo lathu akutichepela - NEEF appeared first on Malawi 24.