Pomwe nthawi imati 6:30 usiku uno aphungu a kunyumba ya malamulo tsopano adutsitsa ndondomeko ya zachuma ya mchaka cha 2025/2026 yokwana 8.076 trillion Kwacha (K8, 076, 667, 784, 858) yomwe nduna ya zachuma a Simplex Chithyola Banda anapeleka mnyumbayi mwezi watha. Ndalamazi zapita ku ma unduna ndi ku nthambi za boma ndipo aphungu amadutsitsa imodzi […]
The post Aphungu adutsitsa bajeti ya mchaka cha 2025/2026 appeared first on Malawi 24.