Anthu okhala ku dera la Ndirande mu nzinda wa Blantyre ali wefuwefu kusaka madzi odzithira ku nkhope pomwe apolisi akuphulitsa utsi okhetsa misozi ku makomo kwa anthu. Anthu ena adandaulira apolisi kuti ayesetse kupeza njira zina zothamangitsira anthu omwe akuchita ziwonetselozi, poti utsiwu ukufika ku makomo ndipo ati pafupi ndi msika wa Ndirande pali chipatala […]
The post Apolisi aphulitsa utsi okhetsa misonzi ku Ndirande appeared first on Malawi 24.