Boma la Dziko la German lero lapereka ndama zokwana K35 billion zomwe zigwire ntchito ya mtukula pakhomo. Mukulankhula kwawo, nduna yazachuma a Simplex Chithyola Banda adayamika boma la Germany kamba ka thandizo la chuma chochuluka onga ichi. A Chithyola alonjeza dziko la German kuti ligwiritsa ncthito bwino chuma chomwe boma la German lapereka ku boma […]
The post Boma la German lapereka ndalama zokwana K35 billion kudziko la Malawi za mtukula pakhomo appeared first on Malawi Nyasa Times - News from Malawi about Malawi.