Eni minibus atadandaula kuti akumapereka ndalama zambiri kwa eni migodi komanso oitanira, boma lati lichotsa anthuwa m'malo okwelera minibasi. Nduna ya Zofalitsa Nkhani, yemwenso ndi m'meneri wa boma a Gospel Kazako ndi omwe anena izi m'mawa wa lero pa msokhano wa atolankhani Blantyre. Malingana ndi a Kazako, kuyitanila ma minibus kwathetsetdwa komanso zoti ena ndi […]
The post Boma lati lichotsa eni migodi m'malo okwelera minibasi appeared first on Malawi 24.