Pomwe dziko la Malawi likudutsa mu ziphinjo za njala, kusowa kwa mafuta, kusayenda bwino kwa chuma, kuyenda pang'ono pang'ono kwa zitukuko mwa zina, boma lapeza njira ina yogwiritsa ntchito ndalama za misonkho pofokozera aMalawi kudzera ku Hotela ya Golden Peacock momwe Boma likugwilira ntchito mu pologalamu yomwe aMalawi ena ati ndi ya ndale yotchedwa 'Boma […]
The post Boma lisakazanso ndalama zina za misonkho kufotokozera zitukuko kudzera ku hotela appeared first on Malawi 24.