Archbishop wa mpingo wa Katolika mu Archdiocese ya Blantyre, a Thomas Luke Msusa ati chaka chino pokhala chaka cha masankho aMalawi akhalebe aMalawi ndipo alimbane ndi kuchotsa njala ndi umphawi zomwe zakuta dziko lino. Poyankhula kwa Bvumbwe m'boma la Thyolo pa mwambo wa maliro a yemwe anali kazembe wakale Lucius Chikuni yemwenso anali katswiri pa […]
The post Chaka chino ndi cha masankho, tilimbane ndi kuchotsa njala ilipoyi - Msusa appeared first on Malawi 24.