M'tsogoleri wa dziko lino Lazarus Chakwera wadzudzula mchitidwe wa ziwawa omwe unachitika dzulo ku Lilongwe. Iwo apempha apolisi kuti afufuze mwansanga ndikuchitapo kanthu. Kudzera mkalata yomwe yatulutsa nyumba ya chifumu ndipo yasayinidwa ndi m'neneri wa pulezidenti Anthony Kasunda, a Chakwera ati ndi okhudzidwa ndi mchitidwewu chifukwa kuchita zionetsero ndi ufulu wa anthu kotero kusokoneza ufuluwu […]
The post Chakwera wadzudzula mchitidwe wa ziwawa appeared first on Malawi 24.