Timu ya Chelsea usiku uno yakodola timu ya Tottenham Spurs mu mpikisano wa English Premier League (EPL) kuti agumulane masewelo awo a chi nambala 30 pa bwalo la Stanford Bridge mu mzinda wa London. Chelsea yomwe inapita kopumulira (International break) itagonja kangapo, sikuwawonela kukondwa ma timu a Manchester City ndi New Castle omwe ayima kutsogolo […]
The post Chelsea maso ndi maso ndi Tottenham Spurs usiku uno appeared first on Malawi 24.