Usiku wa dzulo Brighton yalongosola nsagwada za Chelsea pozipinda katatu pa bwalo la Falmer mu chikho cha English Premier League (EPL) komwe Chelsea inali alendo. Kaoru Mitoma anakhazika chete Chelsea asanabwere Yonkuba Minteh ndi dzilango dzake dziwiri pa mphindi ya 38 ndi 63 kuti masewelo athe 3-0 kukomela Brighton. Brighton yadzikankha kufika pa ma point […]
The post Chelsea yakunthidwa appeared first on Malawi 24.