Dzulo anthu ena omwe akuganizilidwa kuti ndi a Malawi Congress Party (MCP) anabowola mateyala a galimoto za a Phungu achipani cha Democratic Progressive (DPP). Lero mu nyumbayi aphungu a chipani cha DPP adandaula kuti chitetezo chawo chili pachiwopsezo pa zomwe zinachitika dzulo. A Victor Musowa phungu wa dera la Mulanje Bale ati, anthu omwe anavala […]
The post Chitetezo sichilibwino ku Nyumba ya Malamulo appeared first on Malawi 24.