Anyamata anu mwawatuma ku Tunisia aja afikako koma kwatsala ndikubweletsa zotsatira tsopano. Timu ya dziko lino yampira wamiyendo yatera mdziko la Tunisia lero kudzera pa bwalo la Ndege la Tunis-Carthage International, pomwe ikuchalira kuvungumulana ndi timu ya dzikolo Lolemba lino. Timu ya dziko lino yomwe yanyamuka dzulo, idzikapita pa bwalo la Hammadi Agrebi ikuchokera kosakazidwa […]
The post Flames yafika ku Tunisia appeared first on Malawi 24.