'Kaya ndi kundipha pa zifukwa za ndale andiphe koma sinditopa,' watelo Alfred Gangata yemwe ndi wachiwiri kwa mtsogoleri wa chipani cha Democratic Progressive (DPP) mchigawo cha pakati, pomwe amalankhula pa area 3 mu mzinda wa Lilongwe kutsatira kutulutsidwa kwawo pa belo ya bwalo yomwe oweluza milandu ku bwalo la Lilongwe awapatsa lero. A Gangata omwe […]
The post Gangata wati alibe mantha appeared first on Malawi 24.