Mphunzitsi wa Flames yemwe wangolembedwa kumene Kalisto Pasuwa wayamba ntchito yake ndi chipambano pomwe wawaula Comoros 0-2 mu mpikisano wa African Nation Championship Qualifiers pa bwalo la Bingu mu nzinda wa Lilongwe. Zigoli za Binwell Katinji ndi Zebron Kalima mzigawo zonse ziwiri ndi zomwe zapatitsa ma points onse timu ya Malawi the flames kuti ipite […]
The post Kalisto Pasuwa wayamba kutumikira zofuna aMalawi appeared first on Malawi 24.