Anthu ochita malonda ogulitsa tomato mu msika waukulu mu mzinda wa Blantyre adandaula kamba ka kukwera kwa mitengo yowodera tomato zimene zikuchititsa kuti bizinezi yawo ilowe pansi. Modzi mwa anthu ochita malondawa, Christopher Gama wati tomato akumaoda K220,000 pa Dishi (bikili ya ma litazi 20) kusiyana ndi nthawi zonse pamene amaoda K15,000. Izi zachititsa kuti […]
The post Kukwera kwa mtengo kwa tomato kwakhudzaso anthu ogulitsa appeared first on Malawi 24.