Pakuwoneka panali kusamvana pakati pa apolisi maka pa komwe wachiwiri kwa mtsogoleri wa chipani cha Democratic Progressive (DPP), mchigawo cha pakati, a Alfred Gangata akazengedwere pomwe mlandu wawo awusamutsila ku bwalo la Nkukula ku Lumbadzi m'boma la Dowa. Poyamba a Gangata anafika nawo ku bwalo la milandu la Lilongwe ku area 3 komwe mosakhalitsa ananyamuka […]
The post Kusamvana kwabuka pa mlandu wa Gangata appeared first on Malawi 24.