Aphungu ochuluka achizimayi ndi ena aamuna Lero atuluka mnyumba ya Malamulo kuwonetsa mkwiyo wawo pomwe ati Nyumba ya Malamulo sikuwathandiza a Grace Kwelepeta omwe ndi phungu wa dela la Zomba Malosa ndipo galimoto lawo linabowoledwa mateyala ndi kuphwanyidwa nyali ndi anthu omwe ati anavala makaka a chipani cha Malawi Congress (MCP) mwezi watha. A Kwelepeta […]
The post Kwelepeta adandaulira Nyumba ya Malamulo za kuchedwa kuwathandiza pa kusweka kwa galimoto lawo appeared first on Malawi 24.