Anthu a m'mudzi mwa Ng'onga, mfumu yaikulu Nsamala m'boma la Balaka ayamba m'bindikiro pa ofesi ya bwanamkubwa wa bomali ati pofuna kukakamiza unduna wa maboma ang'ono kuti usamutse bwanamkubwa wa bomali, Tamanya Harawa. M'modzi mwa akuluakulu omwe akonza m'bindikiro wu, Armson Kabvalo wati akuchita izi potsatira kutha kwa masiku asanu ndi awiri omwe anapereka ku […]
The post M'bindikiro pa ofesi ya DC wa boma la Balaka wayambika appeared first on Malawi 24.