Mphunzitsi wamkulu wa timu ya Mighty Wanderers, Bob Mpinganjira watulutsa m'ndandanda otsiliza wa osewela a timuyi okwana 30 omwe wati ndi amene akufuna kutengetsa nawo chikho cha 2025 TNM Super League chaka chino, monga limakhalira khumbo la aliyense. Mpinganjira wayankhula izi pa msonkhano wa atolankhani lero omwe anachititsa ku Lali Lubani mu mzinda wa Blantyre […]
The post Mighty Wanderers yasefa ndikutsala ndi osewela 30 omaliza appeared first on Malawi 24.