Mtsogoleri wa dziko lino Lazarus Chakwera wati nayenso ali ndi mafunso opanda mayankho pa za imfa ya yemwe adali wachiwiri wake a Saulos Chilima pa ngozi ya ndege mu nkhalango ya Chikangawa ngati momwenso Mary, mkazi wa malemuwa, alinso ndi mafunso opanda nawo mayankhowa. Mu uthenga wake lero pomwe amatsekulira nyumba ya malamulo, Chakwera wati, […]
The post Nane sindikudziwa, ndili ndi mafunso opanda mayankho - watelo Chakwera pa za imfa ya Chilima appeared first on Malawi 24.