Ochita malonda ku Ndirande mu nzinda wa Blantyre alengeza kuti mawa achita ziwonetsero posakondwa ndi kukwera mitengo kwa katundu osiyanasiyana zomwe akuti zakhuda malonda awo. Wapampando wa ochita malonda mu nsikawu, Chancy Widon, wauza nyumba zina zofalitsa nkhani kuti iwo akhala akukapeleka madandaulo awo ku khonsolo ya mnzinda wa Blantyre komwenso akakumane ndi bwanamkubwa wa […]
The post Ndirande ilowa m'bwalo mawa appeared first on Malawi 24.