Mzika zina zokhuzidwa zaloza chala m'mwenye ochita malonda a H Adam kuti nyumba zake zikunyatsitsa mzinda wa Zomba popeza ndizosawoneka bwino. Patrick Gama yemwe amachita bizinesi yokonza foni zowonongeka wati pali nyumba zina zomwe zili m'phepete mwa ssewu waukulu ochokera ku Blantyre kupita ku Lilongwe ndizofunika kuzigwetsa ndikumanga zina chifukwa zikunyatsitsa mzinda wa Zomba. Iye […]
The post Nyumba za Adam zikunyasitsa mzinda wa Zomba - zatero mzika zokhudzidwa appeared first on Malawi 24.