Mkulu wa bungwe loona za ufulu wa anthu la Centre for Human Rights and Rehabilitation (CHRR), Michael Kaiyatsa wapempha anthu m'dziko muno kuti apewe m'chitidwe ophana ponena kuti aliyense ali ndi ufulu okhala ndi moyo. Kaiyatsa wanena izi kutsatira kukula kwa chiwerengero cha imfa zodza kamba kophedwa, pomwe posachedwapa apolisi ku Mponera m'boma la Dowa […]
The post Oganizilidwa pa milandu yakupha adzitengeledwa ku khothi mwansanga - Kaiyatsa appeared first on Malawi 24.