N'kuthekadi kuti chitsime chimadziwika ndi chakuya pamene chaphwera, chifukwa a Malawi ochuluka akuti bola kwa Farao komwe kuja. Ulendo wa ku Kenani ati aulephera ndipo iwo ndi okonzeka kubwelera. Mtsogoleri wa kale a Peter Mutharika akuoneka ali ndi chikoka chochuluka pakati pa a Malawi ndipo anthu ochuluka ati iwo pokaponya voti azangopita kukachonga pa a […]
The post Okonda a Chakwera yang'anani kumbali: a Malawi ochuluka akufuna APM abwelere appeared first on Malawi 24.