Public Affairs Committee (PAC) yalimbikitsa zipani kuti zizichita kampeni ya mtendere pamene dziko la Malawi likuyembekezeka kuchititsa zisankho zapatatu pa 16 September chaka chino. Izi zadziwika Lachinayi pamene PAC idakumana ndi mtsogoleri wa chipani chotsutsa cha Democratic Progressive (DPP), a Arthur Peter Mutharika kunyumba kwawo m’boma la Mangochi. Motsogozedwa ndi wapampando wa komitiyi Monsinyu Patrick […]
The post PAC ikumana ndi APM appeared first on Malawi 24.